Andy P

0
119

Zina langa ndiine Reauben. A. Putire. Ndimakhala Blantrye kubangwe B. C. A Kwamakolo anga ndi ku zomba chingale TA Mlumbe m’mudzi mwa Ndasaliranji Ndinayamba zoimba mu chaka cha 2014.

Nthawi imeneyo ndili ku school ndima friends tikumaimba ma desk komano sikiti tinkazitengera kwambiri ayi cox ndinkaziona ngati zochedza kenako ndinayamba kumazipanga record ndekha paden that tym tinali ndi pc yomwe tinkagwilitsa tchito koma zinali zija zomangokhala ngati poswelapo.

So in 2015 ndinafika Blantrye & ndinakumana ndi munthu yemwe tinaziwana kwambiri nayeso amaimba atanva mene nane ndimapangila anandilimbikitsa wow mfana u got a talent utha kuimba zokoma heavy ukufunika kumavaya ma studio abho ine owo okay? Chabwino ndinabwelera kwathu ku nzomba 2016 nafikaso Blantyre kubangwe koma ndimakhala pano ndiyamba kuimba first session ndinakaimba ku matrix records producer wake Sispence.

I was featured that song with Levitiko & M double ma guys atafila anandilimbikitsa heavy ine nayamba kulimbikila & now I got a fans cause ndimalimbikila kukakha heavy padakali pano I have a lot of project okwana 11 komaso soon ndikhalanso ndikutulutsa nyimbo ina yomwe ndaimba ndi Original Passenger. Ndinasakha kumaimba nyimbo za uzimu kwaine nachitenga cha mtengo wapatali kutumikila Mulungu kuzera mu nyimbo. Zikomo

Team umafuna chani music

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here