[Lyrics] Blakjak Feat. Dav Risen x Dare Devils – Mula

0
208

Intro (Marcus)
Yoh!You know’!!Martin Anjelz!Pali akazi ena amafuna kuti azikanakana Koma ali ndi anzawo ooneka bwino ndi maSistezi ooneka bwino, Ine nnaonapo situation imeneyi
Martin let me tell you something man

VERSE ONE (Marcus)
Ndili ndi zofooka zambiri ndikudziwa
Koma nah Mkazi kundikana ndikuDiwa
Kapena apo ayi kumwa mowa ndikuwiwa
Koma wait paja ali ndi nzake Tapiwa [Mwasintha nthawi yomweyi?]

Paja sindimachedwatu
Ngati asali Nzako olo masteni adyedwatu
Sindiona size mphamvu kubedi amwedwatu
Mwachidule ukandikana ine pachematu

Siine hule koma kuti ndili pa stress
Ndipo ndiulule mumabwerekana ma dress
Naye imamukhala imamatchama ndi purse
Ndiye decision yokanayo pangani reverse

HOOK
Ndizakusandutsa Nazo Mula
Ukafuna Uzidhulaa
Uzangodabwa Ndagwira Nzako
Kapena Sister Wako (Repeat)

CHORUS
Tsono Babe Zili Ndi Iwee (eh eh eh eh)
Zili Ndi Iwee (eh eh eh eh)
Zili Ndi Iwee (eh eh eh eh)
Kuti Undikane Kaya Undilore (Iwe)

VERSE TWO (Blakjak)
Ufuna nzichita kumakunyengelera
Zomwezi nzichita Kumakuchondelera
Adah, Khala Ndi Kukongola kwakoko Wandimva
Zoti Ndimakufuna zijanso Ndagiver/

Ndinkafuna udzadye Nawo Chuma (Chuma)
Koma udachulutsa phuma (phuma)
Unkandiyesa Ndine Owawa
Koma Azinzakowa amadziwa ndimakoma/

Pano NdikuVaiba ndi Sister Wako
Ndikumamvananso ndi Nzako
Nde Iwe Ukafuna Uzidhula
Ndikuchotsa Pa Mahope pa, Ndizakusandutsa Nazo Mula/

HOOK
CHORUS

VERSE THREE (GD)
Ukhale plan B kapena Plan A
Ukhale mumumu kapena ukhale bae
It’s up to you am in your life baby either way
TadziDula Am here to stay Tidzikumanabe/

Lord knows my weakness crazy about your thickness
Now peep this Nde ukamadzimva u princess
I turn your friends or your sis into a witness
Show her a good time then she tells you the business/

Ndidzimumkwela ngati taxi taxi
Nde zidzikupwetekela pansi pansi
Ukadzafuna kubwelera no tchansi tchansi
Nde kuli bwino ulole basi basi/

HOOK
CHORUS

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here