[Lyrics] Blakjak – Mtima Wache

0
61

Intro
Yeah
Heeee
Mtima wache nde mbeee
blakjak (indeee)

Verse 1
Kodi ndimalakwa Chani
Nnalakwira Ndani
Man Vuto lanu Kodi nchani
Mtimawu munatengela Ndani
Ndisachite chinthu mupeke Nkhani
Kodi mumapindulapo Chani
Amakulipirani Ndi ndani
Mtimawu Munautenga Kwani
Aaah Inu man Tandiuzani
Ndichiyani Chomwe sinkupangilani
Kapena Mwina Nnakulakwirani
Ngati ndinalakwa aaah Pepani

Hook
Nanga Zonse ndingapange basi Agende
Chilichose Ndingapeze basi Atenge
Akufuna Nzivutika Kuti Akondwee
Choncho Basi, Mtima Wache Nde Mbeee

Chorus
Basi
Mtima Wache Nde Mbeee (Indee)
Basi
Mtima Wache Nde Mbeee
Akufuna Nzivutika Kuti Akondwee
Choncho Basi Mtima Wache Nde Mbeee (×2)

Verse 2
Ndakuuza Ndayamba Kuhopela Ka Flora
Basi Nawe Uli Konko Kukandikhobola
Nanga Ndikanakuuza Kuti Wandilora
Simpaka Khosi Mukanamuthyola
Dzanadzanali Ndakuuza Ka Secret
Kungofika Lero Nkhani Ili Public
Kodi Man Khalidwe ilili ndi Litiliti
Kapena Mwina Wina ndi Ufiti
Aliyense Pano Akudabwa
Kupanda Kunyoza Wina Mumamva Kuyabwa
Olo Nzoyamwila Kuchoka Kobadwa
Mukanazitolera Man Mukuchedwa

Hook
Nanga Zonse ndingapange basi Mugende
Chilichose Ndingapeze basi Mutenge
Mukufuna Nzivutika Kuti Mukondwee
Choncho Basi, Mtima Wache Nde Mbeee

Chorus
Basi
Mtima Wache Nde Mbeee (Indee)
Basi
Mtima Wache Nde Mbeee
Akufuna Nzivutika Kuti Akondwee
Choncho Basi Mtima Wache Nde Mbeee (×2)

Bridge
Mtima Wache Nde
Mtima Wache Nde
Mtima Wache Nde
Mtima Wache Nde Mbeee (×4)

Chorus
Basi
Mtima Wache Nde Mbeee (Indee)
Basi
Mtima Wache Nde Mbeee
Akufuna Nzivutika Kuti Akondwee
Choncho Basi Mtima Wache Nde Mbeee (×2)

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here