[Lyrics] Eli Njuchi Feat. Gwamba – Nawe (Lero)

0
811

Intro
Yoh yoh (Yoh yoh yoh)
Njuchi (Exclusive)

Chorus
Lero ndiyenda nawe (Nawe nawe nawe)
Kuli konse ndiyenda pambali nawe (Nawe nawe nawe)
Lero ndiyenda nawe (Yeah yeah yeah)
Mawa usimba lokoma podzuka nane

Verse 1 (Eli Njuchi)
Ima ndisambe (n’sambe)
Boyfriend anunkhile (n’khile n’khile n’khile)
Ima nditchene (n’tchene)
Boyfriend awusosole
Ngati wakonzeka tiye
Ndavala those shoes that you bought me
You smell so nice you
You look so nice you (why)

Chorus
Lero ndiyenda nawe eh
Kuli konse ndiyenda pambali nawe eh (why)
Lero ndiyenda nawe eh
Mawa usimba lokoma podzuka nane eh (why)

Lero ndiyenda nawe nawe (ndiyenda ndiyenda, why)
Lero ndiyenda nawe nawe (ndiyenda ndiyenda, why)

Verse 2 (Gwamba)
Eyoh Eli!

Yoh, Mu bhafa ndi khalamo half an hour
Ukukhafa? ine singati mafanawa (heh)
Kuvaya city mall ntakugwila dzanja
Ex wako ankakukisa ngati ganja (Ha ha ha)
Kukukonda mpaka kuthawa
kugwila lero kwanu kuonekela mawa
Nanga ya lobola? ndili nayo
Mkazi kudabwa ng’ombe 50 zili kwawo (Ma ma ma)
Za ma looks zo taleka
Landlord kuwona mpaka kukwela temper
Nde chonde uzipezeka
Ndiyamba kuyenda chokwawa ukamandizemba
Uku ma DJ, uku dinner (aarh)
Wamasuka ndakuwona ukuvina (aarh, heh)
Za manyazi-zo zitaye
Kuli konse utavaye ndili nawe (why)

Chorus
Lero ndiyenda nawe eh
Kuli konse ndiyenda pambali nawe eh (why)
Lero ndiyenda nawe eh
Mawa usimba lokoma podzuka nane eh (why)

Lero lero nawe nawe (ndiyenda ndiyenda, why)
Lero lero nawe nawe (ndiyenda ndiyenda)

 

 

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here