[Lyrics] Ho Wo Kire – Panado Cover

0
115

Composed by: Onesimus Muzik
Re-arranged by: HO WO Kire
Beat Cover by: Thewz G
Produced by: Lonje Lonje TakTic Damba
Performed by: HO WO Kire

Intro…
Yeyah 247…. Haaa!!
Amakonda mijedooo, amakondwa munthu azingoliraaa
Zochitika ngati okhwimilaa / daily daily bize ntopola
Kubaya ma inchesiii/ kuupasa moyo wanga businessiii
Machitidwe ake aujudasi/ makhalidwe awo ndianjenjete

Chorus
Amafuna ndi kokoloke, amakhumbila ndita kokoloka
Amafuna ndi sokoloke, amafuna mwina nditakomoka X2
NSANJE APASE PANADOL …… AMWEKO PANADOL
NSANJE ANINKHEE PANADOL …… AMWEKO PANADOL

Verse 1 (Rap)
These niggaz r trying to piss on me/ but I don’t give a damn cuz gist on me
In the mind what they wish me bad / All they want is to see me cry
Ndima guy ausilu/ they don’t know peace or know how to chill
Akufuna ndi kokoloke, njeee/ akufuna ndisokoloke, njeee
Cholinga ineyo ndendivutike, AH!/ ana angawa abalalike, AAAH!
Aponda mwala/ Jahjah waine samaiwala
Angondipasapo madalitso, yeah/ kundikhutulira chimdalitso, straight

 Verse 2
They dont wanna see me work hard/ akufuna ine ndizipempha
Samafuna ndiyendele njale /NO! samakondwa ndikamadya money, NO!
Kuzolowera moyo wawutinti tonto/ kufuna kundibera atchuke iwowo
Mafana ausilu/ ntchito kutolatola nkumayenda usiku
Shaaa, kundionongera plan/ Anzanu amakhala kuti anasova masamu
Next big deal, igwereko muline/ komano this thing ndendiyochosana vibe
moyo wachigawenga ochoselana life / Eishhhh zochosana vibe X2

Chorus
Amafuna ndi kokoloke, amakhumbila ndita kokoloka
Amafuna ndi sokoloke, amafuna mwina nditakomoka X2
NSANJE APASE PANADOL …… AMWEKO PANADOL
NSANJE ANINKHEE PANADOL …… AMWEKO PANADOL

End

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here