[Lyrics] Khingi – Chida Changa

0
49

Intro
Waaargee ukuziwa ndili ndi chida chachikulu?
chi guitar chinachake ndimakamenyela ku band inayake
Khingi yuh know

Verse 1
Tsiku lina lake nditasuta bandii
Nnakumana ndi mkazi dzina Brandina
Nnamuuza kuti ndimayimba band
Osadziwa iye wazitengela pa ntima
Last week ndikudutsa pakwawo
Ndamumva akuuza anthu akwawo
Mukadzaona zii ndidzakhala kwa adah awo
Ati amaimba band ali ndi chida chawo
Dzulo chamma 6 ndangomva odi
Ndine Brandina, Khingi alipo kodi
Paja munkati mumaimba band,
Tulutsani chida tifeele ma chord

Chorus
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Makutu ake amafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Makutu ake amafeela chida changa

Verse 2
Ihiiii!
Brandina ati basi sachoka pa deni
After ndaimba chida changa 10
Akuti ndikumampanga entertain
Akufuna chida changa again and again
Akuti imakoma kumvera guitar yangayi
Potakasa nsambo sindimagwera mphwayi
Ndipo akudzimva kuti ndiwa mwai
Brandina sakufuna guitar inanso ayi
Akuti tseke tseke angomva tseke tseke
Ndikamadina nsambo angomva tseketseke
Akuti tseketseke angomva tseketseke
Ndikamatakasa nsambo angomva tseketseke

Chorus Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Makutu ake amafeela chida changaFuna
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Makutu ake amafeela chida changaFuna

Back To Verse 1

Chorus Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Makutu ake amafeela chida changaFuna
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Akufuna atafeela chida changa
Makutu ake amafeela chida changaFuna

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here