[Lyrics] Khingi – Second Wave

0
44

INTRO
Khingi yuh know! kom’badadabang!
You know me!

CHORUS
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave

Ine ndimamuna olimbikila olo kwa chaka ndidikila

VERSE ONE
Ine ndi philimoni nkhakamila banda
Sindimaopa olo bebi ya kumpanda
Olo ndili pa zero ndikungokanda
Ndimalimbikila bebi ikhale yanga
Kundikana kamodzi ndimabweranso
Pa gate yakwanu ndi matha kusweranso
Ma braz ako kundiphika ndimadzelanso
man ah nuh romeo koma chikondi ti mafelanso
Mmh

BRIDGE
Sindiopa mkazi akatchena
Ndimatsatira zomwe soldier ananena

VERSE TWO
Anthu akundinena ati poti ndine bilidala
Iwe mu motor ine kuguza wilibila
Akuti zinazi ndisamaziyambile dala
Koma ndimakufeela sindingakusiye dala
Ukhale trap queen ine wako king kong
ngakhale sindichokela ku dingdong
Phone yanga yophwasuka ilibe ringtone
Me nuh go play wit your heart like a ping pong
Mmh

BRIDGE
Sindiopa mkazi akatchena
Ndimatsatira zomwe soldier ananena

CHORUS
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave
Ine ndimamuna olimbikila olo kwa chaka ndidikila
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave

REPEAT VERSE ONE
Ine ndi philimoni nkhakamila banda
Sindimaopa olo bebi ya kumpanda
Olo ndili pa zero ndikungokanda
Ndimalimbikila bebi ikhale yanga
Kundikana kamodzi ndimabweranso
Pa gate yakwanu ndi matha kusweranso
Ma braz ako kundiphika ndimadzelanso
man ah nuh romeo koma chikondi ti mafelanso
Mmh

CHORUS
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave
Ine ndimamuna olimbikila olo kwa chaka ndidikila
Ukandikana ndidzabwera ndi second wave, second wave

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here