[Lyrics] Nyasa Guruz – Elube

0
26

Intro
Blakjak
Yo! Class Is Permanent!
Original Nyasa Guruz!
N dot Y dot G!!!!!!!!

Verse 1
Pappa
M’mawa amangodzuka (Elube!)
Akununkha thukuta
Ndikungodzipuputa
Ndagoma naye Elube

Blakjak
Elube Why? Elube What? Elube How? Elube Who?
You Such a Disgrace to your body
Now you wonder why the people talk about you
Yuh fi Take Care of yo body

Jinke
Perfume alibe kanthu
Ngati sumasamba thupi lako lonse ndithu
Zozolazola zonse Elube
Sizikongoletsa thupi iwe umve
Uve,
Uvewoo

Hook
Elube dziwa kuchapa(Elube!)
Elube dziwa kusamba(Elube!)
Shower! (Elube!)
Bafa! (Elube!)
Nkhani ndiyako Elube!!
(Nkhani ntaunimu ndiyako iwe Elube)

Verse 2
Jinke
Ukamayenda panseu ngati zenizeni
Zovala sumachapa iwe nchani kwenikweni
Model wanji opanda nkhope yeniyeni
Vula chigoba tikuoneko weniweni

Badde
Let me tel yu som’gyal
Zovala uzichapa bwino
Kumaziviyika mu sopo
Kukungolako ndi ntchito
Osati kujambula ma photo

Blajak
Munthu Wanji, Ooneka Bwino kunja Kokha
Kukhala Kodalira ma Make Up
Chewali Wanga udzimva Aah
Usamatengeke ndi U Diva Aah

Hook

Verse 3
Pappa
Mkazi wapfungo! mkazi wapfungo!
Amabwenzeretsa chitukuko mbuyo
Pitani uko! pitani uko!
Munthu wamoyo kununkha ngati zifuyoooo!

Blakseed
Maluzi asakhale excuse
Kuoneka bwino don’get it confused
Mkazi wabwino ama..!
Valanso bwino kunu!….nkhilanso bwino
Kukwecha mano onse mbee!

Not an easy life to be a diva
Makamaka ukakhalanso opanda zida
Pachabe ukhonza kungotenga mbimba
Ma looks or no looks chemwali osagiver ee!

Hook*3

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here