
Artist: Peoples Emcee Feat. Ill Mind
Title: Msasewere
Album: 3F Free From Fear
Release Date: 31st July, 2020
Intro
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
PreChorus
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mafana Mafana
Paulimbo sasewera
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mafana Mafana
Padiwa sasewera
Chorus
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mwaona liti kuwala
Kodi mukufuna kukudeleni
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
Verse 1 (Peoples Emcee)
Whoooo Yeah
Fire blaze
Kutentha nju
Ahot fire can’t cool
How gon you stand the heat
Ndi mastyle a plastic
Fake colors don’t stick
See they fade quick
Just be true
Get out the blur
Take it easy mafana
Zofuna zamoyo sizikwana
Osapanga chibwana
Chinabala mwana
I’m so Japan mfana osaka
Dzuwa linyenga
Mdima usaka
Kwanunkwanu nthengo ndalaka njoka
Osanyoza komwe unachoka
Poti unachoka
Ukuziputira tsoka
Dziko la tsoka
Tsiku ndilimodzi udzachoka
Osapanga chibwana mchombo lende
Mbalame thu mwala umodzi nkati ndigende
Nyenyezi yoshuta
Father God mfana wachauta
Bows and arrows chimfana chauta
36 Chambers chimfana cha wu tang
Yankhotakota kumangopota
Pre Chorus
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mafana Mafana
Paulimbo sasewera
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mafana Mafana
Padiwa sasewera
Chorus
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mwaona liti kuwala
Kodi mukufuna kukudeleni
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
Verse 2 (ILL Mind)
Nyimbo zanu ndimangomva pokoso
Mumachulutsa makani mukangonenya timatokoso
Mukanapolako moto
Im living my dreams ndili mmaloto
More action kuchepetsa mtokoto.
See the flames tayatsa moto
Muli pagolo mumenya mamoto
Flow yaukulali
Mfana ometa mmbali mbali
Ndili Ku thug kudya ma beat
Condenser ya gono ndi mbale
Flow ya yes yes ya ginger
Skill yosowa ya uninja
Pa beat ine ndi masinja
Check 808 chikusinja
Ndili pa easy kugwetsa mabars
Rapper wakoyo kumudya ndi madalazi
Kumudya osaphika ndikasaladi
I got goals ndimascora
Ine ndi mor saradi
Bridge (Peoples Emcee & ILL Mind)
Mafana msasewere
Mafana mafana
Paulimbo sasewera
Mafana msasewere
Mafana Mafana
Padiwa sasewera
PreChorus
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mafana Mafana
Paulimbo sasewera
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mafana Mafana
Padiwa sasewera
Chorus
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
Mwaona liti kuwala
Kodi mukufuna kukudeleni
Mafana Mafana Mafana
Msasewere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
See the flames of fire
Kodi mukufuna mupsyerere
Get the whole EP here
Peoples Emcee – 3F Free From Fear EP