[Lyrics] Peoples Emcee – Pamene Paja

0
80

Artist: Peoples Emcee
Title: Pamene Paja
Album: 3F Free From Fear 
Release Date: 31st July, 2020

Intro
Hear hear hear hear

Chorus
Mbala inadza
Kuba
Kupha
Ndikuwononga
Mwana wamunthu anadza
Kufunafuna ndikupulumutsa chotaikacho

Verse 1
Kunali chinkhondo mwamba pamenepaja
Owukirayo nathothedwa pamenepaja
Tsoka mtunda ndi nyanja pamenepaja
Oyipayo watsikira konko pamenepaja
Makolo mmundamo pamenepaja
Chinjoka ndi mkazi pamenepaja
Chipatso pakati pa munda kudyedwa pamenepaja
Chabwino ndi choipa pamenepaja
Makolo ochimwa m’bando ochimwa
Kuphedwa koyamba pachibale pamenepaja
Mwazi panthaka pamenepaja
Lilaka lonama pamenepaja
Imfa pamenepaja
Yalowa aah

Chorus x2
Pakuti mbala inadza
Kuba
Kupha
Ndikuwononga
Mwana wamunthu anadza
Kufunafuna ndikupulumutsa chotaikacho

Verse 2
Moyo osatha kubedwa pamenepaja
Moyo osatha kuphedwa pamenepaja
Moyo osatha kuononengedwa pamenepaja
Imfa kolowa pamenepaja
Olema ndi othodwa pamenepaja
Moyo ovuta pamenepaja
Zowawa kulowa pamenepaja
Kuwawa kawawa pamenepaja
Zovuta kuvuta pamenepaja
Mavuto osatha pamenepaja
Munda wabwino pamenepaja
Mbeu zabwino kufetsedwa pamenepaja
Tiligu ndi nansogole pamenepaja
Tidzaona pokolora pamenepaja

Chorus x4
Mbala inadza
Kuba
Kupha
Ndikuwononga
Mwana wamunthu anadza
Kufunafuna ndikupulumutsa chotaikacho

Hear hear hear hear

Get the whole EP here
Peoples Emcee – 3F Free From Fear EP

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here