
Artist: Peoples Emcee
Title: Zanga Zonse
Album: 3F Free From Fear
Release Date: 31st July, 2020
Intro
Hear hear hear
Light vision
I told you man
Chorus
Palibe chomwe ndinakubisira
Zanga zonse ndinakuululira
Zinanso zomwe ndinazikwirira
Ndinakufukurira
Zanga zonse ndinakuulurira
Verse 1
Mbambadi mtheladi
Ndazindikiradi
Kuti mwa iwedi
Mulibedi choonadi
Palibe anakudzodza
Ndiwe wamabodza
Chinyengo unatsongoza
Zoona sutha kuloza
Nanga ndi chani kufuna kuipatsa mbiri yanga
Kodi ndikulakwa kuziwako zanga
Kodi ndikulakwa kukupasako danga
Mmoyo mwanga
Kusunga milandu
Ndiwe waupandu
Kundiweluza pomwe siwe oweluza
Moti undigwire dzanja
Ukufuna kunditaya Ku nyanja
Kusokoneza zomwe mmutu mwanga ndinasanja
Cholinga kufuna kundipenda kundiimika pa nsanja
Cholinga kufuna kundipenda kundiimika pa nsanja
kodi ndikulakwa kukupasako iwe danga mmoyo wanga
Chorus
Palibe chomwe ndinakubisira
Zanga zonse ndinakuululira
Zinanso zomwe ndinazikwirira
Ndinakufukurira
Zanga zonse ndinakuulurira
I don’t trust in ou
I don’t count on you
I don’t trust in you
I don’t count on you
Verse 2
Nanga ndichani kupanga zoyalutsa
Nanga ndichani mzimu wanga kusautsa
Chakudya mudyo osautsa
Ndiwe osautsa
Kufuna chuma changa chonse kundisautsa
Malo anga kufuna kundisamutsa
Kundisamutsa
Kundisamutsa
Kundisamutsa
Told you I know I’m a born sinner
But I believe I’m a winner
On my goals sinchitira mwina
Better now than tsiku lina
Took you around
Show you background
The foundation I built on
To bring it on
I made you part of my team
Shared with you the dream
Made you part of my team
Shared with you the dream
Chorus
Palibe chomwe ndinakubisira
Zanga zonse ndinakuululira
Zinanso zomwe ndinazikwirira
Ndinakufukurira
Zanga zonse ndinakuulurira
I don’t trust in you
I don’t count on you
I don’t trust in you
I don’t count on you
Get the whole EP here
Peoples Emcee – 3F Free From Fear EP