[Lyrics] Recall – Stick Pon Line

0
86

INTRO
RECALL, MWAMPHAMVUSO, FROM A TO ZO,
MI TALK IT SO,
ONE TING MI KNOW IN LIFE,
YOU’VE BE TRUE TO YOURSELF,
YOU AFFI STICK PON LINE, NO OTHER WAY

CHORUS
UKHOZA KUFIKA POMWE UMALOTA
UKHOZA KUFIKA POMWE UMAFUNA
UKHOZA KUPEZA ZOMWE UMAKONDA
YOU BETTER STICK PON DI LINE

VERSE 1
PHIKA MAGANIZO, KULA
NKHAWA ZAKO KWA MULUNGU TULA
SATANA, ASAKUMATE IWE PHULA
ATATE, MWANA, MZIMU WOYERA TCHULA
NGATI UFUNA ZAKO ZIKUYENDERE
MWALA WOGUDUBUKA SUNGAYANGE NDERE
POMWE UNAPATA IWE GWIRITSA
ANZAKO ALIBE NGAKHALE KACHIDUTSWA

CHORUS
UKHOZA KUFIKA POMWE UMALOTA
UKHOZA KUFIKA POMWE UMAFUNA
UKHOZA KUPEZA ZOMWE UMAKONDA
YOU BETTER STICK PON DI LINE

VERSE 2
FUNIRA ZABWINO NGAKHALE ANZAKO
NDIPOMWE UPEZA MADALITSO AKO
NTHAWI IKANALIPO CHITA ZAKO
LIMBIKA POGWIRA NTCHITO ZAKO
NGATI ZAKUVUTA, IWE FUNSA
NJIRA TIMADZIWA NDI KUFUNSA
MACHEZA ACHIBWANA IWE CHEPETSA
DZUDZULA, PHUNZITSA, DZIWITSA

CHORUS
UKHOZA KUFIKA POMWE UMALOTA
UKHOZA KUFIKA POMWE UMAFUNA
UKHOZA KUPEZA ZOMWE UMAKONDA
YOU BETTER STICK PON DI LINE

VERSE 3
WORK HARDER MAN NO OTHER WAY
WIPE ALL YOUR TEARS AND STAND FIRM
MAN AFFI HUSTLE MONEY EVERYDAY
EVERY MICKLE MAKE AH MUCKLE STAND STILL
EVEN THE LIFE GWAAN ROUGH AND TOUGH
NAH WAITING HEAR MAN DEM JOKES
BELIEVE ADDITEACHA NAH GO LIKE THAT
MI BUILD SONGS, BUY HOUSE, BUY CLOTHES AND CAR

CHORUS
UKHOZA KUFIKA POMWE UMALOTA
UKHOZA KUFIKA POMWE UMAFUNA
UKHOZA KUPEZA ZOMWE UMAKONDA
YOU BETTER STICK PON DI LINE

VERSE 4
PHIKA MAGANIZO, KULA
NKHAWA ZAKO KWA MULUNGU TULA
SATANA, ASAKUMATE IWE PHULA
ATATE, MWANA, MZIMU WOYERA TCHULA
NGATI UFUNA ZAKO ZIKUYENDERE
MWALA WOGUDUBUKA SUNGAYANGE NDERE
POMWE UNAPATA IWE GWIRITSA
ANZAKO ALIBE NGAKHALE KACHIDUTSWA

CHORUS
UKHOZA KUFIKA POMWE UMALOTA
UKHOZA KUFIKA POMWE UMAFUNA
UKHOZA KUPEZA ZOMWE UMAKONDA
YOU BETTER STICK PON DI LINE

(kuimba mwamphamvu)

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here