[Lyrics] Vitu Marley – Wachiona Ndani

1
72

Malcolm X’s “ballot or the bullet” speech

Verse 1
Ndipatseni chi ndime, ndilime ndi lirime
Always calm on a track, iyi ndufuna ndililime
I don’t believe in tongues, ndiyankhulabe malirime
Ku Nsanje-ka mpakana ku Paris andimve
Timkati zinthu zisintha after kulowa chilimwe
Koma pokolola misale mbanje yobzala ya mzimbe
Chilichonse chinakwela ndi Bola yokha siinasinthe
Olo ku Limbe pano tungovala zilimbe
System ndi wachiona ndani
Namvelako Matafale so I know olakwa ndani
It’s the same shit, changosintha ndi chimbudzi
Pamasintha sipali bho, bola ndikafere kumudzi
Ngakhale Pali owina koma palibe oluza
Akapita Ku parliament amasanduka otsutsa
Ukaonetsetsa and if you understand this
Onsewa ndi amodzi moti ndi wachiona ndani

Chorus
Akakhala pa mkhate sapheka
Akakhala Chagaga sachedwa
Kuti udziwa-Satta uchedwa
Anthuwa ndi amodzi, ukaonetsetsa (ndi)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (Wachiona Ndani)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (wachiona Ndani)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (wachiona Ndani)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (wachiona Ndani)

Verse 2
Pena ndekha ndekha ndikadekha
Music yaku Malawi ndikamayiwerenga
Amene amaitsata hip hop ndi ochepa
Call me a hater kaya muziti ndima jela
Ena anangogwera kweni ndi ambwelera
Lyrically ali under ngati Herrera
Ndikawerenga, amakwana seven or more
Achina (King K) come on now you already know
Kell kay sandiwaza, komabe ndabwera ndi nkhani
Ma rappers ambiriwa ndia wachiona nda
Amadziwana ndi uje, lende amawakankha
Koma pansi pa mtima, timadziwa samatha
Olo mtakumana nawo singapereke sawatcha
Olo atafuna beef, ine olo yosawotcha
Lirime langa nde lupanga, ukapanga chibwana
Ndidzakukapa kapa nga a chacha

Chorus
Akakhala pa mkhate sapheka
Akakhala Chagaga sachedwa
Kuti udziwa-Satta uchedwa
Anthuwa ndi amodzi, ukaonetsetsa (ndi)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (Wachiona Ndani)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (wachiona Ndani)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (wachiona Ndani)
Wachiona Ndani wachiona Ndani (wachiona Ndani)

Verse 3
Pamene ndikukula, daily ndimadzifunsa
Kodi ndidzapita kuti ndikadzati ndaduwa
Kodi dzasanduka nyenyezi mwina kapena maluwa
Kapena waku Moto n’kudzasanduka phulusa
So ndidafunsa a shehe, ndidafunsa ansembe
Koma pamafunso anga yankho sinalipeze
So ndidafunsa abusa, chilungamo cha yeshua
Koma poyankha pawo I swear sanali sure
Now am focused on my goals, siinenso chipuwa
Ena apembedza mwezi, ena amapembedza dzuwa
So namufunsa Merry, chilungamo chama Rasta
Jane anandiyankha ndiyekhayo ali ndi Ansah
Pano ndidamudziwa Garvey, ndidamudziwa Selassie
I am who I am nde osamanditchura Ras
Coz ukaonetsetsa and if you overstand this
Onsewa ndi amodzimodzi poti ndi wachiona ndani

 

 

1 COMMENT

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here